Salimo 60:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tithandizeni kuti tichoke m’masautso,+Pakuti chipulumutso chochokera kwa munthu wochokera kufumbi n’chopanda pake.+ Salimo 118:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuthawira kwa Yehova n’kwabwino+Kusiyana ndi kudalira munthu wochokera kufumbi.+ Salimo 146:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamakhulupirire anthu olemekezeka,+Kapena mwana wa munthu wina aliyense wochokera kufumbi amene alibe chipulumutso.+
11 Tithandizeni kuti tichoke m’masautso,+Pakuti chipulumutso chochokera kwa munthu wochokera kufumbi n’chopanda pake.+
3 Musamakhulupirire anthu olemekezeka,+Kapena mwana wa munthu wina aliyense wochokera kufumbi amene alibe chipulumutso.+