Numeri 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madzi a tembererowa alowe m’matumbo mwako kuti akatupitse mimba yako ndi kufotetsa ntchafu yako.” Ndipo mkaziyo aziyankha kuti: “Zikhale momwemo! Zikhale momwemo!”* Machitidwe 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 (Chotero munthu ameneyu, anagula+ munda ndi malipiro a ntchito zosalungama.+ Anagwa chamutu+ n’kuphulika mimba, moti phokoso la kuphulikako linamveka, ndipo matumbo ake onse anakhuthuka.
22 Madzi a tembererowa alowe m’matumbo mwako kuti akatupitse mimba yako ndi kufotetsa ntchafu yako.” Ndipo mkaziyo aziyankha kuti: “Zikhale momwemo! Zikhale momwemo!”*
18 (Chotero munthu ameneyu, anagula+ munda ndi malipiro a ntchito zosalungama.+ Anagwa chamutu+ n’kuphulika mimba, moti phokoso la kuphulikako linamveka, ndipo matumbo ake onse anakhuthuka.