2 Mafumu 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komabe, anaumirira osasiya kuchita machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anachimwitsa+ nawo Isiraeli. Salimo 109:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene akulimbana ndi ine avale manyazi,+Ndipo adziphimbe ndi manyaziwo ngati akudziphimba ndi malaya akunja odula manja.+
3 Komabe, anaumirira osasiya kuchita machimo a Yerobowamu+ mwana wa Nebati, amene anachimwitsa+ nawo Isiraeli.
29 Amene akulimbana ndi ine avale manyazi,+Ndipo adziphimbe ndi manyaziwo ngati akudziphimba ndi malaya akunja odula manja.+