-
Yobu 12:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Iye amanyoza anthu olemekezeka,+
Ndipo amakhwepetsa lamba wa anthu amphamvu.
-
Yeremiya 13:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 ‘Ine ndinachititsa nyumba yonse ya Isiraeli ndi nyumba yonse ya Yuda kundimamatira+ mofanana ndi mmene lamba amagwirira m’chiuno mwa munthu,’ watero Yehova. ‘Ndinachita zimenezi kuti iwo akhale anthu anga,+ akhale dzina langa lotchuka,+ anditamande ndi kukhala chinthu changa chokongola. Koma iwo sanandimvere.’+
-
-
-