Deuteronomo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu. Salimo 119:135 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 135 Ndikomereni mtima ine mtumiki wanu,+Ndipo ndiphunzitseni malamulo anu.+ Yeremiya 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno mogwirizana ndi malamulo ndi malangizo, ndinatenga chikalata cha pangano chomata ndi chosamata.+
4 “Tsopano inu Aisiraeli, mverani malangizo ndi zigamulo zimene ndikukuphunzitsani kuti muzitsatira. Mukatero mudzakhala ndi moyo+ n’kukalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu akukupatsani, ndi kukalitenga kukhala lanu.
11 Ndiyeno mogwirizana ndi malamulo ndi malangizo, ndinatenga chikalata cha pangano chomata ndi chosamata.+