Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+ Salimo 104:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwakhazikitsa dziko lapansi pamaziko olimba.+Silidzagwedezeka mpaka kalekale, mpaka muyaya.+ Mlaliki 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’badwo umapita+ ndipo m’badwo wina umabwera,+ koma dziko lapansi lidzakhalapobe mpaka kalekale.*+
93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+