Salimo 78:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Anayamba kumanga malo opatulika ngati malo okwera a paphiri,+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+ Salimo 104:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwakhazikitsa dziko lapansi pamaziko olimba.+Silidzagwedezeka mpaka kalekale, mpaka muyaya.+ Salimo 119:90 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+
69 Anayamba kumanga malo opatulika ngati malo okwera a paphiri,+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+
90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+