Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Munthu wochoka pa njira yochita zinthu mozindikira,+ adzapumula mumpingo wa anthu akufa.+

  • Mateyu 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pa nthawi imeneyo Yesu ananena kuti: “Ndikutamanda inu Atate pamaso pa onse, Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa mwabisira zinthu zimenezi anthu anzeru ndi ozindikira ndipo mwaziulula kwa tiana.+

  • Mateyu 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma iye anawayankha kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira zinsinsi zopatulika+ za ufumu wakumwamba, koma anthu amenewa sanapatsidwe mwayi umenewo.+

  • Luka 2:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Tsopano patapita masiku atatu, anamupeza ali m’kachisi,+ atakhala pakati pa aphunzitsi. Anali kuwamvetsera ndi kuwafunsa mafunso.

  • 2 Timoteyo 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera amene angathe kukupatsa nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke+ kudzera m’chikhulupiriro chokhudza Khristu Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena