Salimo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zingwe za imfa zinandikulunga,+Chikhamu cha anthu opanda pake chinali kundiopseza.+ Chivumbulutso 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+
15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+