Ekisodo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Agwiritseni ntchito yakalavulagaga anthu amenewa ndipo muonetsetse kuti sakuchita ulesi ndi kumvera zabodza.”+ 1 Samueli 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo m’dziko lonse la Isiraeli munalibe wosula zitsulo. Izi zinali choncho chifukwa Afilisiti anati: “Aheberi asasule lupanga kapena mkondo.”+
9 Agwiritseni ntchito yakalavulagaga anthu amenewa ndipo muonetsetse kuti sakuchita ulesi ndi kumvera zabodza.”+
19 Ndipo m’dziko lonse la Isiraeli munalibe wosula zitsulo. Izi zinali choncho chifukwa Afilisiti anati: “Aheberi asasule lupanga kapena mkondo.”+