-
Nehemiya 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Iye anayamba kuuza abale ake+ ndi gulu lankhondo la ku Samariya kuti: “Kodi Ayuda ofookawa akuchita chiyani? Kodi akuona ngati akwanitsa chintchito chomanga chimenechi? Kodi adzapereka nsembe?+ Kodi amaliza kumangako tsiku limodzi? Kodi adzachita kufukula miyala imene inatenthedwa ndi kuigwiritsiranso ntchito?”+
-