Ekisodo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+“Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+ Oweruza 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mvetserani mafumu inu,+ inunso nduna, tcherani khutu:Ine ndidzaimbira Yehova, ndithu ndidzamuimbira.Ndidzaimbira Yehova, Mulungu wa Isiraeli,+ nyimbo zomutamanda.+
15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+“Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+
3 Mvetserani mafumu inu,+ inunso nduna, tcherani khutu:Ine ndidzaimbira Yehova, ndithu ndidzamuimbira.Ndidzaimbira Yehova, Mulungu wa Isiraeli,+ nyimbo zomutamanda.+