Salimo 56:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amandiukira ndi kundibisalira,+Iwo nthawi zonse amaonetsetsa mmene ndikuyendera,+Pamene akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+ Salimo 120:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimalimbikitsa mtendere,+ koma ndikalankhula,Iwo amafuna nkhondo.+
6 Amandiukira ndi kundibisalira,+Iwo nthawi zonse amaonetsetsa mmene ndikuyendera,+Pamene akundidikirira kuti awononge moyo wanga.+