Salimo 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mudzandiwonjola mu ukonde umene anditchera,+Pakuti inu ndinu malo anga achitetezo.+ Salimo 71:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni m’manja mwa woipa,+Ndipulumutseni m’manja mwa munthu wochita zinthu mopanda chilungamo komanso mopondereza.+
4 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni m’manja mwa woipa,+Ndipulumutseni m’manja mwa munthu wochita zinthu mopanda chilungamo komanso mopondereza.+