Salimo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso anga amayang’ana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+ Salimo 91:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iye adzakupulumutsa mumsampha wa wosaka mbalame,+Ndi ku mliri wobweretsa masautso.+ Mateyu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musatilowetse m’mayesero,+ koma mutilanditse kwa woipayo.’+
15 Maso anga amayang’ana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+