Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 malinga ndi mwambo wa ansembe, inali nthawi yake yakuti azilowa m’nyumba yopatulika ya Yehova,+ n’kupereka nsembe zofukiza.+

  • Chivumbulutso 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Atatenga mpukutuwo, zamoyo zinayi ndi akulu 24 aja+ anagwada ndi kuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze woimbira+ ndi mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. Zofukizazo+ zikuimira mapemphero+ a oyera.

  • Chivumbulutso 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mngelo wina anafika ndi kuimirira kuguwa+ lansembe. Iye anali ndi chiwiya chofukiziramo chagolide, ndipo anamupatsa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide, limene linali pamaso pa mpando wachifumu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena