Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+ Chivumbulutso 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo, utsi wa zofukizazo unakwera pamaso pa Mulungu kuchokera m’dzanja la mngeloyo limodzi ndi mapemphero+ a oyera.
2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
4 Pamenepo, utsi wa zofukizazo unakwera pamaso pa Mulungu kuchokera m’dzanja la mngeloyo limodzi ndi mapemphero+ a oyera.