Salimo 113:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dzina la Yehova lidalitsike,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+ Salimo 146:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+
2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+