Salimo 103:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova wakhazikitsa mpando wake wachifumu kumwamba.+Ndipo ufumu wake ukulamulira chilichonse.+ Salimo 111:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zochita zake+ n’zaulemerero ndi ulemu,+ו [Waw]Ndipo chilungamo chake chidzakhalapobe kwamuyaya.+