-
Yesaya 14:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Izi ndi zimene ndatsimikiza kuchitira dziko lonse lapansi, ndipo ili ndi dzanja limene latambasuka kuti likanthe mitundu yonse ya anthu.
-
-
Danieli 4:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Inuyo adzakuthamangitsani pakati pa anthu ndipo muzidzakhala pakati pa nyama zakutchire.+ Muzidzadya udzu ngati ng’ombe+ ndipo muzidzanyowa ndi mame akumwamba. Ndiyeno padzadutsa nthawi zokwanira 7+ kufikira mutadziwa kuti Wam’mwambamwamba ndiye Wolamulira wa maufumu a anthu,+ ndiponso kuti akafuna kupereka ulamuliro kwa munthu aliyense, amamupatsa.+
-