Salimo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amadziwa njira za olungama,+Koma oipa adzatheratu pamodzi ndi njira zawo.+ Miyambo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma oipa adzachotsedwa padziko lapansi+ ndipo achinyengo adzazulidwamo.+