Salimo 86:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sangalatsani mtima wa ine mtumiki wanu,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu Yehova.+ Salimo 143:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti ndimadalira inu.+Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+
8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti ndimadalira inu.+Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+