2 Mafumu 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+ Salimo 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+Zimenezi zinditsogolere.+Zindifikitse kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+ Salimo 86:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+
3 “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+
3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+Zimenezi zinditsogolere.+Zindifikitse kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+
11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+