2 Samueli 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ komanso kuti wamukwezera+ ufumu wake chifukwa cha anthu ake Aisiraeli.+ Salimo 89:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti inu ndinu amene mumachititsa mphamvu zawo kukhala zaulemerero.+Ndipo mwa kukoma mtima kwanu, nyanga* yathu imakwezedwa.+
12 Davide anadziwa kuti Yehova wachititsa kuti ufumu wake ukhazikike mu Isiraeli,+ komanso kuti wamukwezera+ ufumu wake chifukwa cha anthu ake Aisiraeli.+
17 Pakuti inu ndinu amene mumachititsa mphamvu zawo kukhala zaulemerero.+Ndipo mwa kukoma mtima kwanu, nyanga* yathu imakwezedwa.+