1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+ Salimo 75:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu akuti:* “Ndidzadula nyanga zonse za anthu oipa.”+Koma nyanga za munthu wolungama zidzakwezedwa.+ Salimo 92:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma inu mudzakweza nyanga* yanga ngati nyanga ya ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+Ndidzadzola mafuta abwino.+ Salimo 132:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ku Ziyoniko ndidzakulitsa nyanga* ya Davide.+Wodzozedwa wanga ndamukonzera nyale.+
10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+
10 Mulungu akuti:* “Ndidzadula nyanga zonse za anthu oipa.”+Koma nyanga za munthu wolungama zidzakwezedwa.+
10 Koma inu mudzakweza nyanga* yanga ngati nyanga ya ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+Ndidzadzola mafuta abwino.+