Salimo 31:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mudzandiwonjola mu ukonde umene anditchera,+Pakuti inu ndinu malo anga achitetezo.+ Salimo 91:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iye adzakupulumutsa mumsampha wa wosaka mbalame,+Ndi ku mliri wobweretsa masautso.+ Salimo 124:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Moyo wathu uli ngati mbalame imene yathawa+Pamsampha wa munthu wogwiritsa ntchito nyambo.+Msamphawo wathyoka,+Ndipo ife tapulumuka.+ 2 Timoteyo 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso kuti mwina nzeru zawo zingabwereremo kuti awonjoke mumsampha+ wa Mdyerekezi, poona kuti wawagwira amoyo+ pofuna kukwaniritsa cholinga chake.
7 Moyo wathu uli ngati mbalame imene yathawa+Pamsampha wa munthu wogwiritsa ntchito nyambo.+Msamphawo wathyoka,+Ndipo ife tapulumuka.+
26 Komanso kuti mwina nzeru zawo zingabwereremo kuti awonjoke mumsampha+ wa Mdyerekezi, poona kuti wawagwira amoyo+ pofuna kukwaniritsa cholinga chake.