Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Zitatero akazi anayamba kuuza+ Naomi kuti: “Adalitsike Yehova,+ amene wachititsa kuti usasowe wokuwombola lero, kuti dzina lake lifalitsidwe mu Isiraeli.

  • 1 Samueli 25:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndiyeno Davide anamva kuti Nabala wamwalira. Atatero, iye anati: “Adalitsike Yehova amene wandiweruzira mlandu+ ndi kundimasula ku chitonzo+ cha Nabala, komanso wagwira ine mtumiki wake kuti ndisachite choipa.+ Yehova wabwezera zoipa za Nabala pamutu pake!”+ Pamenepo Davide anatumiza anthu kuti akamufunsirire Abigayeli, kuti akhale mkazi wake.+

  • Salimo 68:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Adalitsike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+

      Mulungu woona wa chipulumutso chathu.+ [Seʹlah.]

  • Luka 1:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena