Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 ukamvetsera nzeru ndi khutu lako,+ ukaika mtima wako pa kuzindikira,+

  • Miyambo 3:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mwana wanga, zimenezi zisachoke pamaso pako.+ Usunge nzeru zopindulitsa ndiponso kuganiza bwino,+

  • Miyambo 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amanyoza mnzake,+ koma munthu wozindikira bwino ndi amene amakhala chete.+

  • Danieli 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 amene analibe chilema chilichonse,+ ooneka bwino, ozindikira zinthu, anzeru,+ odziwa zinthu, omvetsa zinthu mwamsanga,+ amenenso akanatha kutumikira m’nyumba ya mfumu.+ Anawabweretsa kuti awaphunzitse kulemba* ndiponso chinenero cha Akasidi.

  • Mateyu 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena