Deuteronomo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+ Afilipi 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+
5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+
15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+