Miyambo 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 kuti kukuteteze kwa mkazi woipa,+ komanso ku lilime losalala la mkazi wachilendo.+ Miyambo 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mkaziyo wamusocheretsa mnyamatayo pochita zinthu zambiri zomukopa.+ Wamunyengerera ndi milomo yake yotulutsa mawu okopa.+
21 Mkaziyo wamusocheretsa mnyamatayo pochita zinthu zambiri zomukopa.+ Wamunyengerera ndi milomo yake yotulutsa mawu okopa.+