Miyambo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kudzakupulumutsa kwa mkazi wachilendo, mkazi wochokera kwina+ wolankhula mwaukathyali,+ Miyambo 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kuti utetezedwe kwa mkazi wachilendo,+ ndiponso kwa mkazi wochokera kwina amene amalankhula mawu okopa.+
5 kuti utetezedwe kwa mkazi wachilendo,+ ndiponso kwa mkazi wochokera kwina amene amalankhula mawu okopa.+