Deuteronomo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azim’kwapula+ pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikoti zogwirizana ndi choipa chimene wachita. Miyambo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa kulipiritsa munthu wonyoza, wosadziwa zinthu amakhala wanzeru.+ Munthu wanzeru akapatsidwa malangizo, amadziwa zinthu.+ Miyambo 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Thamangitsa wonyoza, kuti mikangano ithe ndiponso kuti milandu ndi kunyozedwa zilekeke.+
2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azim’kwapula+ pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikoti zogwirizana ndi choipa chimene wachita.
11 Mwa kulipiritsa munthu wonyoza, wosadziwa zinthu amakhala wanzeru.+ Munthu wanzeru akapatsidwa malangizo, amadziwa zinthu.+