Miyambo 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamilomo ya munthu womvetsa zinthu pamapezeka nzeru,+ koma ndodo amakwapulira msana wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+ Miyambo 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zilonda zobwera chifukwa chomenyedwa zimachotsa zoipa,+ ndipo zikwapu zimafika mpaka mkatikati mwa mimba.+ Miyambo 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chikwapu n’cha hatchi,+ zingwe n’za pakamwa pa bulu,+ ndipo ndodo ndi yokwapulira msana wa anthu opusa.+ Aheberi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ngati mawu amene angelo ananena+ analidi osagwedezeka, ndipo pa tchimo lililonse ndi kusamvera kulikonse, chilango chinaperekedwa mogwirizana ndi chilungamo,+
13 Pamilomo ya munthu womvetsa zinthu pamapezeka nzeru,+ koma ndodo amakwapulira msana wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+
30 Zilonda zobwera chifukwa chomenyedwa zimachotsa zoipa,+ ndipo zikwapu zimafika mpaka mkatikati mwa mimba.+
3 Chikwapu n’cha hatchi,+ zingwe n’za pakamwa pa bulu,+ ndipo ndodo ndi yokwapulira msana wa anthu opusa.+
2 Pakuti ngati mawu amene angelo ananena+ analidi osagwedezeka, ndipo pa tchimo lililonse ndi kusamvera kulikonse, chilango chinaperekedwa mogwirizana ndi chilungamo,+