Miyambo 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 umphawi wako udzabwera ngati wachifwamba,+ ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+ Miyambo 24:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 umphawi wako ndithu udzabwera ngati wachifwamba ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+ 2 Atesalonika 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso, pamene tinali ndi inu, tinali kukupatsani lamulo ili:+ “Ngati wina sakufuna kugwira ntchito, asadye.”+
11 umphawi wako udzabwera ngati wachifwamba,+ ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+
34 umphawi wako ndithu udzabwera ngati wachifwamba ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+
10 Ndiponso, pamene tinali ndi inu, tinali kukupatsani lamulo ili:+ “Ngati wina sakufuna kugwira ntchito, asadye.”+