Miyambo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+ Miyambo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho moyo wake ulibe chilichonse.+ Koma anthu akhama adzanenepa.+ Miyambo 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso waulesi pa ntchito yake+ ndiye m’bale wake wa munthu wobweretsa chiwonongeko.+ Miyambo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha kuzizira, waulesi salima.+ Iye azidzapemphapempha nthawi yokolola koma sadzapatsidwa kanthu.+
4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+
4 Chifukwa cha kuzizira, waulesi salima.+ Iye azidzapemphapempha nthawi yokolola koma sadzapatsidwa kanthu.+