Miyambo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti amadya mkate wa zoipa+ ndipo amamwa vinyo wachiwawa.+ Miyambo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Madzi akuba amatsekemera,*+ ndipo mkate wakudya mwakabisira umakoma.”+