Salimo 37:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+ Miyambo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ukachita zimenezi udzamvetsa zinthu zolondola, zolungama, zowongoka, ndiponso njira yonse ya zinthu zabwino.+
37 Ona munthu wosalakwa ndipo yang’anitsitsa munthu wolungama,+Pakuti tsogolo la munthu ameneyu ndi lamtendere.+
9 Ukachita zimenezi udzamvetsa zinthu zolondola, zolungama, zowongoka, ndiponso njira yonse ya zinthu zabwino.+