Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+ Mlaliki 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+ Mateyu 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova, kapena akachita lumbiro lodzimana,+ asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Achite malinga ndi mawu onse otuluka pakamwa pake.+
6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+
33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+