Salimo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+Ndipo khazikitsani wolungama.+Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+ Salimo 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.+
9 Chonde, thetsani kuipa kwa anthu oipa,+Ndipo khazikitsani wolungama.+Mulungu pokhala wolungama+ akuyesa mtima+ ndi impso.+