Luka 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene anali kunena mawu amenewa, mayi wina m’khamu la anthulo anafuula n’kumuuza kuti: “Ndi wodala mayi+ amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!”
27 Pamene anali kunena mawu amenewa, mayi wina m’khamu la anthulo anafuula n’kumuuza kuti: “Ndi wodala mayi+ amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!”