Luka 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ali mkati molankhula zimenezi, mayi wina mʼgulu la anthulo anafuula nʼkumuuza kuti: “Wosangalala ndi mayi amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:27 Yesu—Ndi Njira, tsa. 176 Nsanja ya Olonda,5/1/1989, tsa. 208/15/1988, tsa. 8
27 Ali mkati molankhula zimenezi, mayi wina mʼgulu la anthulo anafuula nʼkumuuza kuti: “Wosangalala ndi mayi amene mimba yake inanyamula inu ndiponso amene munayamwa mabere ake!”+