1 Mafumu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi. Yobu 42:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova anadalitsa+ kwambiri mapeto a Yobu kuposa chiyambi chake+ moti iye anakhala ndi nkhosa 14,000, ngamila 6,000, ng’ombe 2,000 zimene zinkagwira ntchito zili ziwiriziwiri, ndi abulu aakazi 1,000. Miyambo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’nyumba ya munthu wolungama muli katundu wambiri,+ koma katundu wa munthu woipa amabweretsa tsoka.+
23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.
12 Yehova anadalitsa+ kwambiri mapeto a Yobu kuposa chiyambi chake+ moti iye anakhala ndi nkhosa 14,000, ngamila 6,000, ng’ombe 2,000 zimene zinkagwira ntchito zili ziwiriziwiri, ndi abulu aakazi 1,000.
6 M’nyumba ya munthu wolungama muli katundu wambiri,+ koma katundu wa munthu woipa amabweretsa tsoka.+