Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+ Miyambo 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 pakuti zimenezi zili ngati nkhata ya maluwa yokongola pamutu pako,+ ndi mkanda wokongola m’khosi mwako.+ Miyambo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usadzudzule wonyoza kuti angadane nawe.+ Dzudzula munthu wanzeru ndipo adzakukonda.+
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+
9 pakuti zimenezi zili ngati nkhata ya maluwa yokongola pamutu pako,+ ndi mkanda wokongola m’khosi mwako.+