Mateyu 5:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde, ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi,+ pakuti mawu owonjezera pamenepa achokera kwa woipayo.+ Yakobo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma koposa zonse abale anga, lekani kulumbira, kaya motchula kumwamba kapena dziko lapansi kapena lumbiro lina lililonse.+ Koma tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi, kuti musaweruzidwe.+
37 Tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde, ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi,+ pakuti mawu owonjezera pamenepa achokera kwa woipayo.+
12 Koma koposa zonse abale anga, lekani kulumbira, kaya motchula kumwamba kapena dziko lapansi kapena lumbiro lina lililonse.+ Koma tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi, kuti musaweruzidwe.+