Salimo 137:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumeneko, amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Ndipo otinyozawo anatipempha kuti tiwasangalatse.+ Iwo anati:“Tiimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni.”+ Mlaliki 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi yolira+ ndi nthawi yoseka.+ Nthawi yolira mofuula+ ndi nthawi yodumphadumpha mosangalala.+
3 Kumeneko, amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Ndipo otinyozawo anatipempha kuti tiwasangalatse.+ Iwo anati:“Tiimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni.”+