Miyambo 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamilomo ya munthu womvetsa zinthu pamapezeka nzeru,+ koma ndodo amakwapulira msana wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+ Miyambo 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kudzudzula kumam’fika pamtima munthu womvetsa zinthu,+ kuposa kukwapula munthu wopusa zikwapu 100.+ Miyambo 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale utasinja chitsiru mumtondo ndi musi limodzi ndi mbewu, uchitsiru wake sungachichokere.+ 1 Akorinto 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi mukufuna chiyani? Mukufuna ndibwere kwa inu ndi chikwapu,+ kapena ndi chikondi ndi mzimu wofatsa?+ 2 Akorinto 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso ndife okonzeka kupereka chilango pa aliyense wosamvera,+ inuyo mukadzasonyeza kuti ndinu omvera pa chilichonse.+
13 Pamilomo ya munthu womvetsa zinthu pamapezeka nzeru,+ koma ndodo amakwapulira msana wa munthu wopanda nzeru mumtima mwake.+
10 Kudzudzula kumam’fika pamtima munthu womvetsa zinthu,+ kuposa kukwapula munthu wopusa zikwapu 100.+
21 Kodi mukufuna chiyani? Mukufuna ndibwere kwa inu ndi chikwapu,+ kapena ndi chikondi ndi mzimu wofatsa?+
6 Komanso ndife okonzeka kupereka chilango pa aliyense wosamvera,+ inuyo mukadzasonyeza kuti ndinu omvera pa chilichonse.+