Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ine ndidzakukanani,* ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+

  • 2 Mafumu 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yehova anali atachititsa anthu a mumsasa wa Asiriyawo kumva+ phokoso la magaleta ankhondo, phokoso la mahatchi, ndi phokoso la gulu lalikulu la asilikali amphamvu.+ Choncho anthuwo anauzana kuti: “Taonani! Mfumu ya Isiraeli yaitanitsa mafumu a Ahiti+ ndi mafumu a Iguputo+ kuti abwere kudzamenyana nafe!”

  • Salimo 53:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Nthawi yomweyo anagwidwa ndi mantha aakulu,+

      Ngakhale kuti panalibe chochititsa mantha.+

      Pakuti Mulungu adzamwaza mafupa a aliyense womanga msasa kuti akuukireni.+

      Isiraeli adzawachititsa manyazi pakuti Yehova wawakana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena