Miyambo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira. Miyambo 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Munthu amene khutu lake limamvetsera chidzudzulo+ chopatsa moyo, amakhala pakati pa anthu anzeru.+ 1 Akorinto 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndikulankhula nanu ngati anthu ozindikira.+ Dziwani nokha zimene ndikunena.
9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira.
31 Munthu amene khutu lake limamvetsera chidzudzulo+ chopatsa moyo, amakhala pakati pa anthu anzeru.+