Salimo 39:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa kudzudzula cholakwa, mwawongolera munthu,+Ndipo mwawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete*+ imachitira.Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ [Seʹlah.] Miyambo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti lamulolo ndilo nyale,+ ndipo malangizo ndiwo kuwala,+ komanso kudzudzula* kowongola zolakwa ndiko njira yamoyo,+ Miyambo 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wonyalanyaza malangizo amasauka ndipo amadzichotsera ulemu.+ Koma amene amamvera chidzudzulo ndi amene amalemekezedwa.+
11 Mwa kudzudzula cholakwa, mwawongolera munthu,+Ndipo mwawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete*+ imachitira.Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ [Seʹlah.]
23 Pakuti lamulolo ndilo nyale,+ ndipo malangizo ndiwo kuwala,+ komanso kudzudzula* kowongola zolakwa ndiko njira yamoyo,+
18 Munthu wonyalanyaza malangizo amasauka ndipo amadzichotsera ulemu.+ Koma amene amamvera chidzudzulo ndi amene amalemekezedwa.+