Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndinene za lamulo la Yehova.

      Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+

      Lero, ine ndakhala bambo ako.+

  • Mateyu 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye adzabereka mwana wamwamuna, ndipo dzina lake udzamutche Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa+ anthu ake+ ku machimo awo.”+

  • Yohane 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Atate saweruza munthu aliyense, koma wapereka udindo wonse woweruza kwa Mwana,+

  • Machitidwe 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiponso chipulumutso sichipezeka mwa munthu wina aliyense, pakuti palibe dzina lina+ pansi pa thambo, limene laperekedwa kwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”+

  • Afilipi 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ngakhale kuti iye anali ndi maonekedwe a Mulungu,+ kukhala wolingana ndi Mulungu sanakuganizirepo ngati chinthu choti angalande.+

  • 1 Timoteyo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti pali Mulungu mmodzi+ ndi mkhalapakati mmodzi+ pakati pa Mulungu+ ndi anthu.+ Ameneyo ndiye munthuyo Khristu Yesu.+

  • Aheberi 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 kumene Yesu, yemwe ndi kalambulabwalo anakalowa chifukwa cha ife.+ Iyeyu wakhala mkulu wa ansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melekizedeki.+

  • Chivumbulutso 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pamalaya ake akunja, ngakhale pantchafu yake, anali ndi dzina lolembedwa lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena